Vote For This Song

Lyrics

UATCHAUYA LYRICS PIKSY x HYPHEN INTRO (PIKSY) Mesa unkati ndine ndekha Mtima wanga sudzasweka Mesa unkati ndine ndekha Mtima wauchekacheka CHORUS Kukukonda ndakhaula Kamtsinje kanga kauma Wandiothetsa mbaula Oh my oh my Uatchauya Kukukonda ndakhaula Kamtsinje kanga kauma Wandiothetsa mbaula Oh my oh my Uatchauya VERSE ONE (PIKSY) Mesa unkati ndine ndekha Mtima wanga sudzasweka Mesa unkati ndine ndekha Mtima wauchekacheka Eeh Wandimeta mpala Wandidyetsa mpunga wa miyala Wandigulula mano Wachiphwasula chipangano Wandipatsa theche ngati moni Wandipatsa usiku ngati morning Wandikwera pa mutu ngati Drone Wandilakwira opanda sorry CHORUS Kukukonda ndakhaula Kamtsinje kanga kauma Wandiothetsa mbaula Oh my oh my Uatchauya Kukukonda ndakhaula Kamtsinje kanga kauma Wandiothetsa mbaula Oh my oh my Uatchauya VERSE TWO (HYPHEN) Maonekedwe ndi ngelo Pakamwa nde pa munthu wa ndale Kamunthu kodzadza ndi chinyengo Zitheka bwanji mu tea kuthiramo Achale Kundipatsa madzi momwera ziweto Ndachezera kuothera nyale Shaa Wandigwiritsa wire wa EGENCO Chiletso, kususa pansi utachotsa mbale Wandiphwetsa chidale Ka mtima kanga kukaika apo Kutengana ndi anzako, busy kusewera chandamale Iwe si munthu wamba Ngati unafika poyimeta nkhanga Olo maula ikunana Iwe nde umadziwa kulanga Ambiri akukamba PIKSY Wandiotchera msika Wandilanda cha mzika Wandibwiritsa Paprika Nsima yanga waviika ah BRIDGE (PIKSY & HYPHEN) Mesa unkati ndine ndekha Mtima wanga sudzasweka Mesa unkati ndine ndekha Mtima wauchekacheka CHORUS Kukukonda ndakhaula Kamtsinje kanga kauma Wandiothetsa mbaula Oh my oh my Uatchauya Kukukonda ndakhaula Kamtsinje kanga kauma Wandiothetsa mbaula Oh my oh my Uatchauya

Sharing is cool

You may also like...Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments

From the World

Hits 18687 Plays. | 49433 Downloads.

Recently added songs

Details Votes
Malaj Malaj - Taken ft Princi Musiq & Chizmo Sting (Prod. Gxfted Beats)
Taken (Dancehall)
Dan Lu Dan Lu - Pumani [Tribute] (Prod. Pesi Nyasa Records)
Pumani (Afrobeat)
Teezy Teezy - Panado ft Gentile (Prod. Acoustick & Gentile)
Panado (Afrobeat)
Blaze Blaze - Ungonena Freestyle (Prod. JayDak)
Ungonena (Afrobeat)
Gift Chikaonda Gift Chikaonda - Mwa Inu (feat. Waxy Kay (prod. by Mr Shine)
Mwa Inu (Afro-Pop)
Team Poison Team Poison - Zanga Phee
Zanga Phee (Hip Hop)
Amaro Amaro - Tiyakila Pompa (ft Episodz)
Tiyakila Pompa (Hip Hop)
MJ Kay MJ Kay - One Day
One Day (Hip Hop)
Mwanache Mwanache - Uli Ndi Vuto - [Mwanache & Mr Generator] (Prod. Roy-Viun)
Uli Ndi Vuto (Afrobeat)
Miracle Chinga Miracle Chinga - Mwapambana
Mwapamba (Gospel)

Follow Malawi Music on Instagram